Comments "TIKUDZIWENI - 3 JUNE 2019":
Author: SarrAMalawi sakonda vojambula jambula mwina mukadati muzichita zina zofanafana ndi mbamu
Author: ArazshuraIzo ndi za azungu asiyeni azungu akuguleni ife amalawi ndi DPP yowolayi yakubayi ndalama za zochukazo tizipedza kuti?tidya peint yo?ana akuyenda otsamvala ndiye ndalama yogula pent tiitenga kuti ?
Author: FejindTakunyadilani Mr halah tasilila kwambili more fire
Author: KejasUmphawi mmene wavutila kwathu kuno ndiwochepa kwambiri angakwanitse kugula zimenezo.
Author: ZugorKkkkkk highest and lowest time kkkkkk
Author: Totchakudya chathu ndi siiiiiiiimaaaa nthochi ndi azunguwoooo ogula ziboribori
thoughts on “TIKUDZIWENI - 3 JUNE 2019” Add Yours?